Mayi Lilian Matako, a Ishmael Chitete komanso a Zuberi Chitete akawonekera ku bwalo la milandu Lachiwiri likubwelari komwe akayankhe mulandu opanga zinthu zofuna kuvulaza munthu. Malingana ndi mneneri wa apolisi ku Balaka, Inspector Gladson M’bumpha, anthu atatuwa ali mmanja mwa apolisi powaganizira kuti anathandizana kupeleka chilango chomumangilira mumtengo komanso kumuthira madzi a Chiteze mwana wamkazi […] The post Matako komanso anyamata awiri akawonekera ku bwalo la milandu Lachiwiri appeared first on Malawi 24.
Afrique
Matako komanso anyamata awiri akawonekera ku bwalo la milandu Lachiwiri [Malawi 24]
- Catégorie : Malawi 24