Chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP) chatsimikiza za kutuluka m’chipani kwa a Dalitso Kabambe, koma chati sichikudandaula ponena kuti ngakhale banja limene limatha ndipo aliyese amalowera kwake. Potsatira kalata yomwe a Kabambe omwe anakhalaposo gavanala wa banki ya ikulu ya Reserve atulutsa Lolemba yolengeza za kutuluka m’chipanichi, DPP yalemba pa tsamba lake la fesibuku […] The post Aliyese ali ndi ufulu osintha chipani – yatelo DPP appeared first on Malawi 24.

More at malawi24.com

Abonnez vous à la Newsletter d'Afropages.fr

Inscrivez-vous à notre newsletter et profitez gratuitement d’informations personnalisées sélectionnées avec soin, rien que pour vous !

 

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - Ovh : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023