Wolankhulira Polisi ya Balaka, Gladson M’pumpha watsimikizira nyumba zowulutsa mawu m’dziko muno kuti anthu enanso awiri amangidwa m’mamawa wa Lamulungu kutsatira nkhani yokhudzana ndi mayi Matako omwe anawanjata dzulo chifukwa chozunza mwana wawo wamkazi atampeza kuti anawabera ndalama yokwana K2,000  Anthu omwe anjatidwawa omwe ndipachibale ndi a Ishmael Chitete a zaka 20 ndi Zuberi Chitete […] The post Matako, anthu ena awiri amangidwa pa mlandu wozunza mwana wa zaka 9 appeared first on Malawi 24.

More at malawi24.com

Abonnez vous à la Newsletter d'Afropages.fr

Inscrivez-vous à notre newsletter et profitez gratuitement d’informations personnalisées sélectionnées avec soin, rien que pour vous !

 

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - Ovh : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023