Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati boma lalandira mayankho opatsa chilimbikitso pa nkhani ya kafukufuku wa ngozi yomwe inakhudza wachiwiri wa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima ndi ena asanu ndi atatu.
Afrique
Talandira mayankho opatsa chilimbikitso pa nkhani ya kafukufuku – Kunkuyu [Malawi 24]
- Catégorie : Malawi 24