Bwalo lalikulu lozenga milandu ku Mzuzu lathetsa mlandu omwe limamuzenga Tadikira Mafubza Mutharika komanso anthu ena asanu ndi awiri. Tadikira yemwe ndi mwana wa a Gertrude Mutharika anamangidwa pamodzi ndi anthu asanu ndi awiriwa powaganizira kuti anatengapo gawo pa milandu yozembetsa komanso kupha anthu makumi atatu omwe amaganizilidwa kuti ndi nzika za dziko la Ethiopia […] The post Tadikira tsopano ndi mfulu appeared first on Malawi 24.

More at malawi24.com

Abonnez vous à la Newsletter d'Afropages.fr

Inscrivez-vous à notre newsletter et profitez gratuitement d’informations personnalisées sélectionnées avec soin, rien que pour vous !

 

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - Ovh : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023