Pomwe Mutale Mwanza wanenetsa kuti sanakhalepo pa ubwenzi ndi Tay Grin yemwe akuti ndi khanda komaso samatha kukonda mkazi, “mfumu ya zinyawu-yi” yati ikunong’oneza bondo posavera malangizo omwe anthu ankayipatsa kuti isachite chibwezi ndi nkazi wa ku Zambia-yu.
Afrique
Munandilangizadi aMalawi koma ine kusava – walira Tay Grin [Malawi 24]
- Catégorie : Malawi 24