Aphunzitsi okwana 59 m’boma la Thyolo adandaula kuti bungwe loyendetsa mayeso la MANEB silikuonetsa chidwi chowapatsa ndalama zawo za alawasi pa ntchito yoyang’anira mayeso a JCE, pomwe anzawo ena analandira mayesowa asanayambe kulembedwa.
Afrique
Aphunzitsi ena ku Thyolo sanalandilebe ndalama atayang’anira mayeso a JCE [Malawi 24]
- Catégorie : Malawi 24