‘Thandizani osowa’ – Asilamu apemphedwa pa nyengo yokondwelera Eid Al Adha  [Malawi 24]

Asilamu m’dziko muno awapempha kuti akhale othandiza osowa pomwe akusangala tsiku la Eid Al Adha lomwe amapha ziweto monga mbuzi, ng’ombe ndi nkhosa ndikupereka kwa anthu omwe ali osowa. M’modzi mwa akulu akulu a Bungwe la Bena Charity Trust lomwe ndi la chipembedzo cha chisilamu a Precious Kasopa ndiwomwe ayankhula izi ku Zomba pomwe bungwe’li […] The post ‘Thandizani osowa’ – Asilamu apemphedwa pa nyengo yokondwelera Eid Al Adha  appeared first on Malawi 24.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023