A Dr. Kizito Tenthani tsopano ndi mlembi wa zipani zandale m’dziko muno. Izi zikudza kutsatira kuvomelezedwa kwa a Tenthani pa udindowu ndi nyumba ya malamulo. Potsimikiza za nkhaniyi, m’khalapampando wa komiti yosankha anthu m’maudindo osiyanasiyana a boma ku nyumba ya malamulo a Joyce Chitsulo adati ndi okhutira ndi kusankhidwa kwa a Tenthani pa udindowu ndipo […] The post Dziko la Malawi tsopano Lili ndi mkulu wa kalembera wa zipani watsopano appeared first on Malawi 24.
Afrique
Dziko la Malawi tsopano Lili ndi mkulu wa kalembera wa zipani watsopano (Malawi 24)
- Catégorie : Malawi 24