Mwambo wa maliro a Hope Chisanu uchitika mwezi uno ku America [Malawi 24]

Pomwe anthu akupitilirabe kusonkha ndalama zokwana 43 miliyoni kuti thupi la malemu Hope Chisanu lifike kuno, anthu m’dziko la America atsazikana ndi malemuyu kumapeto a mwezi uno. Chisanu yemwe wasiya mkazi ndi ana awiri, anamwalira Loweluka pa 1 June 2024 atadwala kwa nthawi yochepa m’dziko la America komwe amakhala.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023