Zitsulo kunolana: Bushiri athandiza mneneri Habakkuk kupeza  K1 miliyoni  (Malawi 24)

Khama lipindura: Mneneri Habakkuk yemwe, pafupipafupi, wakhala akupempha Shepherd Bushiri kuti amuthandize ndi K1 miliyoni yokha, waona ngati kutulo pomwe wapatsidwa K6 miliyoni ndi mneneri nzakeyu. Habakkuk yemwe dzina lake lenileni ndi Stanford Sinyangwe, sadzayiwala tsiku La mulungu pa 5 May, 2024  kamba koti mneneri Bushiri anamuchitira chinthu chomwe wakhala akumupempha.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023