Azipita Chamkakala – a mabungwe (Malawi 24)

Atha kuona ma demo angati a Jane Ansah naye Masautso Chamkakala chifukwa a mabungwe ndiye akwiya naye. Ati sakuona phindu lake.  Mabungwe omwe si aboma ati a Chamkala omwe ndi mkulu wa ofesi ya yoyang’anira zozenga milandu m’dziko muno, Director of Prosecutions (DPP), akuyenera kutula pansi udindo polephera kugwira ntchito yake moyenera.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023