Sukula ya sekondale ya Msiki m’boma la Mzimba ikusimba lokoma potsatira thandizo lokwanira 4.3 miliyoni lomwe lalandira kuchokera kwa ophunzira akale pa sukulu yaukachenjede ya Mzuzu. Masiku anayi apitawo, ophunzira akale pa Mzuzu University anadzidzimutsa sukulu ya Msika ndi thandizo la mabuku olemberamo komanso ndalama zimene zigwire ntchito ngati sukulu fizi kwa ana khumi ndi […] The post Sukulu ya Msiki iwomboledwa ndi ophunzira akale apa Mzuzu University appeared first on Malawi 24.
Afrique
Sukulu ya Msiki iwomboledwa ndi ophunzira akale apa Mzuzu University (Malawi 24)
- Catégorie : Malawi 24