Sukulu ya Msika iwomboledwa ndi ophunzira akale pa Mzuzu University (Malawi 24)

Sukula ya sekondale ya Msiki m’boma la Mzimba ikusimba lokoma potsatira thandizo lokwanira 4.3 miliyoni  lalandira kuchokera kwa ophunzira akale pa sukulu yaukachenjede ya Mzuzu.  Masiku anayi apitawo,  ophunzira akale pa Mzuzu University anadzidzimutsa sukulu ya Msika ndi thandizo la mabuku olemberamo komanso  ndalama zimene zigwire ntchito ngati sukulu fizi kwa ana khumi ndi asanu.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023