Chinantindi cha anthu chikupitiriza kutsata ndi kukonda Jetu ngakhale kuti makosana a Podcast Malawi anapereka ganizo lakuti gogoyu asiye kuyimba chifukwa alibe luso pamayimbidwe. Patangopita masiku ochepa chabe a Podcast Malawi chiyakhulireni zokhwatcha Jetu, gogoyu wakatekesa ku sukulu yaukachenjede ya MUBAS mzinda wa Blantyre.
Military affair end goalless (Malawi 24)
18 mai 2024