Mlingo wa madzi mnyanja ya Malawi ukutsika (Malawi 24)

Patapita nthawi ma bizinezi ambiri atasokonekera mmbali mwa Nyanja ya Malawi kamba kakusefukila kwa madzi, a National Water Resources Authority (NWRA) ati tsopano mlingo wa madzi mu mnyanjayi ukuphwera. Malingana ndi mneneri wa bungweli, a Masozi Kasambala izi zikudza kamba koti mvula yomwe imagwa ku Tanzania komanso mchigawo cha ku mpoto kwa dziko lino ikutsika.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023