Makosana a MRA abilibinya Jetu – Dorothy Kingston (Malawi 24)

Dorothy Kingston wadandaula zakhalidwe lomwe achita akuluakulu a Malawi Revenue Authority (MRA) komaso apolisi munzinda wa Lilongwe omwe akuti awazunza komaso kumumenya woyimba wachikulire Jetu. Dorothy yemwe ndi nkazi wake wa woyimba Zeze Kingston, wati gogo wa zaka 72-yu pamodzi ndi iye akumana ndi tsokali Lachinayi madzulo pomwe amabwelera ku Blantyre kuchokera ku Lilongwe komwe […] The post Makosana a MRA abilibinya Jetu – Dorothy Kingston appeared first on Malawi 24.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023